Innocent P. Makuwira
Innocent P. Makuwira - Kwathu Sipadziko songtekst
Je score:
Kwathu sipadziko ndingopitilira; Ndazikundikira chuma kumwambako Mngelo akodola pakhomo lammwamba Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu. Mbuye ndinu bwenzi langa ndithu Ndichitenji ngati kumwambako sikwathu Mngelo akodola pakhomo lammwamba Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu. Mayi watsogola muulemelero Ndifuna kugwira dzanja lake, konko Andiyembekeza chinthuchi ndidziwa Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu