Maskal
Maskal - Ndiwe Wanga songtekst
Je score:
Verse; 1 Pazachikondi chako dziwa ine ndi mboni Sindinalakelake kupita ku Joni Chikondi cha iwe ndi ine sicham'mafoni Nchifukwa sindinapite ku bank kukatenga loan Chikondi chathu chobeba chanoninoni Umandizula moyo ukapereka moni Umandikumbutsa za kwathu kumangoni Ndakondwa umadziwa kuti ine ndi m'goni Chorus*2 Ndiwe wanga ndiwe kuwala kwanga Ndiwe wanga ndiwe nyenyezi yanga Ndiwe wanga ndiwe wanga ndiwe wapamtima wanga Ndiwe wanga ndiwe wanga nyenyezi yanga Ndiwe wanga ndiwe kuwala kwanga Verse; 2 Ndikakha pansi ndimadziwa ndiri ndi mzanga Kuyenda limodzi tifanana mawanga Amandinena ati ndiri nyanga Asatilongoze monga ichita nkhanga Ndithudi ndilonjeza ndzakutengela kunyanja Nthawi imeneyo tikukonzekera banja Ona ambiri akutiombera m'manja Mpakana wena kutimangira nsanja (Back to chorus) Verse; 3 Chikondi chathu chansangala sizachisoni Ena amasangalala akatipatsa moni Unasiya amabenzi onse ndimalinkoni Amatithila madzi ndikumaimba horn Akamadutsa baby, Samamvetsa baby Ngati andale baby, Ali pa njale baby Zimawawawa baby, Kuiwala mawa baby Ngati moyenda baby, Ife tikuyenda baby!, Hee! (Back to chorus till the end)