Langwan Piksy
Langwan Piksy - Maloto songtekst
Je score:
Verse 1 I saw mwana wanga What a cute baby Proud dad anzanga anamva mbebe Kusiyana ndi ana ena iye anali star Ndinagwada kuthokoza Mbuye wodalitsa Tinapita tonse kukagula ma dyper Titagwirana manja pamalo panaipa Tinakula koma we were getting tighter Anthu otiyang'anan amadziwa Timaitha Nkhope yake inali brighter Thupi lake linali lighter Ndi nzeru anamudalitsa Anatengera ine osakaika Ndibwelere ndikagone (heh) Mwina ndingalote nso (heh) Ndingadzamukonde Bola udzandibalire iweyoo Chorus Ndinalota maloto otsekemera ine inde Mwana wanga atafanana nawe Nde nde nde Iwe Ngati ndisadzuke Usadzandikhumudwitse Poti mtima wanga kukhala nawe wavomera Verse 2 Pali ponse Anaoneka akalilombe Ena anakondwa ena sanakondwe Pawirife chikondi chinalipobe Sichinachoke Ndi za mbirimbiri Zotilepheretsa kukhala awiri Tiye tidzikondana mmene tiriri Kunja kuli njoka wanga ndiwe basi Ndikudziwa ndi zotheka eh Kukonda iwe wekha eh Chibwana ndaleka eh Iwe mphete ndikuveka eh Sweetie iwe ndine Mphepo ingawombe tisasinthe Limodzi tiwoloka mitsinje Mpaka tikafike hey Oh babie Chorus Ndinalota maloto otsekera ine inde Mwana wanga atafanana nawe Nde nde nde Iwe Ngati ndisadzuke Usadzandikhumudwitse Poti mtima wanga kukhala nawe wavomera Bridge No pain no gain Kukusiya iwe no ways Ngakhale asakondwe Everything is gonna be okay No pain no gain Kukusiya iwe no ways Ngakhale asakondwe Everything is gonna be okay yeah Chorus Ndinalota maloto otsekera ine inde Mwana wanga atafanana nawe Nde nde nde Iwe Ngati ndisadzuke Usadzandikhumudwitse Poti mtima wanga kukhala nawe wavomera