Langwan Piksy
Langwan Piksy - Uncle Short One lyrics
Your rating:
Chi Piksy Chinfarner Chodziwiker Ndi Boumurr Chorus Hey Uncle Uncle Short-one Mukuganizira zotani Uncle Short-one Kuno ngini yakuphonyani Uncle Short-one Ndikale lija munatchona inu Uncle Short-one Kuno mbumba yakusowani Verse one Maloto awa tinayambira limodzi Sitinaganizire zinthu zingafike chonchi Mmaso mwa ine ya chimwemwe misonzi Oh I wish mukanakhala kuno nkozi My uncle komanso my best friend Munkandiuza chirichonse munali open Ndinkadzanena kwa inu ndikayiputa ndeu Kamunthu kakafupi koma simakani akewo Pena ndimaseka……ndekha Munkati mukakwiya munkadzitchula undertaker Nkhani za inu zambiri zongopeka Pano ndinakula munkathoka ngini yosatheka (Laugh) I called you biggie Munali nane olo weather ingakhale windy Muzambiri munandipanga lead I'm a man now pano ndidziwa zambiri Chorus Verse two Munkanena kuti zinthu zidzayenda One day…. Dollar ndidza spenda Munkanena ndidzaphula if I work hard One day… zakale ndidzagenda Ndikakhala duuu Kukumbuka kale lathu Tinkasowa zinthu Munaganizano zongotuuu... Luka Koma zonse munanena sindinazitaye Ngakhale ngini inashupa sindinagwe mphwayi Mulungu anandidalitsa inakwana nthawi Kunyada kwa abambo anga chimwemwe cha mayi Ngini bho panopa I’m doing awesome Pano ndinapeza aine ma bouncer Pamene pankawopsapo pano ndinadutsa Mulungu anachotsa zonse zinkasautsa Chorus Verse three Ndikasekelera ndinuyo ndimakumbukira Ndikanakondwera mukanakhala mwafupikira Kwa inu… zambiri ndinaphunzira Munkandiuza madalitso adzandikhuthukira Mukanakhalapo mukanamva kukoma Nephew wanu akudziwika ndi boma Anakula pano anapeza kadona Uncle…nephew wanu anablowa Success yanga inabwera ngati heart attack Ndikanena zinthu amayesa ndikulalata Luso lija likumabweretsa dollar Zimene zinkapinga zija Ambuye anathyola Mulungu anatsegula khomo Nephew wanu panopa ndi role model Ndakusowani Uncle Short-one Ndine wanu wanu Langwan Chorus Outro Ndefeyo entertainment