Langwan Piksy
Langwan Piksy - Mphongo lyrics
Your rating:
Chorus Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo) Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo) Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo) Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo) Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo) Verse one Mkazi wanga ndi professional Chikondi chake chiri sensational Chikondi cha natural ma rehearsal no Easy…. Musazitenge personal Lol Chikondi chake ndikuopa chindinenepetsa poti chachuluka starch Kukhala naye sizitheka kungomuyang’ana I’m tempted to touch Ndimadziwa amandikonda asananene akachita kuyankhula nde nanji Chikondi chake ndi more.. Yes I’m feeling all good Chorus Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo) Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo) Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo) Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo) Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo) Verse two Mkazi wanga ali ndi vision Chikondi chake cho no season Amandikonda opanda reason Kusokoneza please no Ndimadziwa kusankha iye kuti akhale wa pa mtima sinnalakwitse yi Zikanakhala zimatheka bwenzi ndikukhala naye like everyday Okambawo amadziwa tilipobe no matter what they gonna say We standing tall, lovings all the way Chorus Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo) Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo) Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo) Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo) Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo) Verse three (Dan lu) Babe mvera ndiwe number one Pagulu la nzako umadya one Ndikumva sugar Ndikumva raga It’s all good (Piksy – rap) Ndine mphongo yowilira Musatsutse ndi mmene ndiku feelira Ondifuna akuyenera kupilira Ndikufewa mafana mwandilira Vomerezani.. Mfana I’m rocking Jus lay back man lemme do the talking Yeah, ndikumva kukoma Chofewa chimphongo chodziwika ndi boma Chorus Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo) Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo) Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo) Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo) Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo)