Langwan Piksy
Langwan Piksy - Bambo Nyimbo lyrics
Your rating:
Verse one – piksy Mmudzi uwu anthu amandikonda kwambiri Amfumu ati ndiime you mp Ati nyimbo za ine ziri amazing Pazokha zitha kukwana kukhala ngati incentive Ku wina you mp no campaign Opikisana nawo akuchita complain Kuchipangitsa Chambo kufeela ngati Ncheni And position yanga ndikuichitabe maintain Mu nyimbomu, ndikondwera mmenemu Kunjoya, kunjoyetsa ena ndikupeza revenue They go hard ndeno I go harder Instrumental kwa ine imagwada Okay, let me take you slow Ndikufuna apa pokha mundimvetse bho Ati zinthu izi ndimazitha bad Bamboo nyimbo, nyimbo zimanditcha dad Bridge Bambo nyimbo Bambo nyimbo uuuh Verse two - piksy Ndimanva kukoma ndikamamenya tune Ochuluka anthu nkumangokuwa nthumwi Ndingati Christmas yomwe yabwera June Ndikaona atsuna akugwedeza fandum Yeah, amanditcha bambo nyimbo Nyimbo so beautiful rainbow ndi symbol Osanama zikuyenda bwino moti Unlike mmbuyo muja pano zafika pa chonchi Bambo nyimbo timenye nanu single Nyimbo yanga mungondimenyera intro Simatama koma kungoyamikira Mmene zinthu zakhalira Madalitso ndalandira Kumenya beats, fans ingofeela Kumenya ma show ma venue kusefukira Wina ndi uyu walowera pa window Ngati ndikunama tandionetse chidindo Mhm anzawo, mukuona bwa? Chorus – jay J Ndimatchedwa anzawo a nyimbo Ndinachokera pa zero Kufika lero kudziwika ndi dziko aaah Ndimatchedwa anzawo anyimbo Ndimatchedwa anzawo a nyimbo Akufuna chimbale kapena single Zokondweretsa kudziwika ndi dziko aaah Ndimatchedwa anzawo a nyimbo Verse three Heh! Ndimatchedwa anzawo a nyimbo Ngakhalenso mithutha inandipatsa udindo It's all good you know zabwino bwino Zonse zikutheka anzawo anyimbo Yo! Tikupanga zen zen Bamboo nyimbo anzawo tikumenya yeni yeni Osafowoka kugwedeza pamalo Ku holda microphone kukuwa ngati mkango Ma guy akudziwa Onse kutifeela Palibe kugonja nonse mukudziwa Kumva kukoma kucheza ah uh Sinthawi yogona no no phada yah! Keep the fire blazing (yah) Moto osazima (yah) Yonse morale Bambo nyimbo, anzawo anyimbo bluh! Chorus – jay J Ndimatchedwa anzawo a nyimbo Ndinachokera pa zero Kufika lero kudziwika ndi dziko aaah Ndimatchedwa anzawo anyimbo Ndimatchedwa anzawo a nyimbo Akufuna chimbale kapena single Zokondweretsa kudziwika ndi dziko aaah Ndimatchedwa anzawo a nyimbo Chorus – piksy Amanditcha bambo Nyimbo Ndinachokera pa zero Kufika lero kudziwika ndi dziko yeah Amanditcha bambo Nyimbo aaah Amanditcha bambo Nyimbo Ndinachokera pa zero Akufufuna chimbale kapena single Zokondweretsa kudziwika ndi dziko aaah Amanditcha bambo Nyimbo