David Kuthyola
David Kuthyola - Matamando lyrics
Your rating:
popeza ndinu oyera ndikhulupira inu tate wa dziko lonse chorus wa zakumwamba ndi zapansi ayenera matamando ine ndikhulupila iye tate wadziko lonse ndiimba matamando ndinu oyera mnjira zonse inu mundiyang'anira masiku amoyo wanga back to chorus