Piksy
Piksy - Angozo lyrics
Your rating:
CHORUS Angozo Safuna zoyambana Angozo Angozo Safuna zokangana Angozo Angozo Angozo Angozo Ndi ntondo ndi ntondo ntondo Angozo Angozo Angozo Ndi ntondo ntondo PIKSY Wodya zake alibe mulandu Ali ndi tsoka wopanga za anthu Zawo zikuyenda Nsanje ndi matenda Zawo amanena ndi anthu Angozo ndi ofewa Angozo sadzatheka Humble, selfless Sathoka za udolo wawo, Ndi katundu, Amfumu Koma mmudzimu akulemera ndani? (Ndi Angozo) Akazi abwino amagomera ndani? (Angozo) Pakati pawo alibe stress ndani? (Ndi Angozo) Ndekuti awa angochedwa kupanga ziphokoso I am the definition of Angozo Chikhala nyerere you know bwenzi ndiri mdzodzo Tsono dzimakomo kutseguka Chikho chawo kusefuka Zowapinga kupatuka Ineyo ndi Angozo CHORUS Angozo Safuna zoyambana Angozo Angozo Safuna zokangana Angozo Angozo Angozo Angozo Ndi ntondo ndi ntondo ntondo Angozo Angozo Angozo Ndi ntondo ntondo TAY GRIN Angozo mdi bad man Wa pa easy koma otchuka ngati Gangnam Ndi ma chick amahita ngati Van Dame Sadzipopa ngati bubble gum Mfana ozitsata (ingofunsafunsa akuuza) Mfana ozisanja (Ona Motor akuphusha) Mfana wa chikoka (Anthu onse mmudzi amamdziwa) Angozo! Olo mafana amatchula dzina Amakwana, amathina Anthu amadziwa ndi makina Mitu yawo imayima Angozo ndi Head-cleaner Dziko limavina Apapa china nchina Ngakhale amene sakufuna apange salute Angozo! CHORUS Angozo Safuna zoyambana Angozo Angozo Safuna zokangana Angozo Angozo Angozo Angozo Ndi ntondo ndi ntondo ntondo Angozo Angozo Angozo Ndi ntondo ntondo LULU Angozo mmudzi nkhani ndi yawo Kulima minda opanda mvula kukolola Angozo mudzi ukamba za iwo Mulungu analemba Angozo ngokolola Ngakhale tsiku la ma dyelero Azimayi amangofuna Angozo ayimbe ng'oma Ena akuti ng'omanso ayi Angozo tiwafuna pafupi ativinitse Kuntero Ngozo ng'oma kuti Booo (Ngozo ayimbe ng'oma oh oh) Kuntero ngozo stepe kuti seee (Ngozo ayimbe ng'oma oh oh) Kuntero Ngozo ng'oma kuti Booo (Ngozo ayimbe ng'oma oh oh) Kuntero ngozo stepe kuti seee (Ngozo ayimbe ng'oma oh oh) Angozo amuna anzawo nsanje Angozo modzichepetsa kuseka Angozo sangamalize chitelera Kuopa kuwadikira pa njira CHORUS Angozo Safuna zoyambana Angozo Angozo Safuna zokangana Angozo Angozo Angozo Angozo Ndi ntondo ndi ntondo ntondo Angozo Angozo Angozo Ndi ntondo ntondo